-
Aheberi 4:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Pakuti mawu+ a Mulungu ndi amoyo+ ndi amphamvu,+ ndipo ndi akuthwa kuposa lupanga lililonse lakuthwa konsekonse.+ Amalasa munthu mumtima mpaka kulekanitsa moyo+ ndi mzimu,+ komanso mfundo za mafupa ndi mafuta a m’mafupa. Mawu a Mulungu amathanso kuzindikira zimene munthu akuganiza komanso zolinga za mtima wake.+
-