Akolose 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Chuma chonse chokhudzana ndi nzeru ndiponso kudziwa zinthu chinabisidwa mosamala mwa iye.+ Akolose 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 chifukwa iye ali ndi makhalidwe onse a Mulungu.+