Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Agalatiya 3:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Khristu anatigula+ nʼkutimasula+ ku temberero la Chilamulo. Anachita zimenezi pokhala temberero mʼmalo mwa ife, chifukwa Malemba amati: “Munthu aliyense wopachikidwa pamtengo ndi wotembereredwa.”+

  • Aheberi 9:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Ndiye chifukwa chake iye ndi mkhalapakati wa pangano latsopano+ kuti anthu amene aitanidwa alandire lonjezo la moyo wosatha.+ Izi zatheka chifukwa cha imfa yake, imene inali ngati dipo lowamasula+ ku machimo amene iwo anali nawo mʼpangano lakale lija.

  • 1 Petulo 2:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Iye ananyamula machimo athu+ mʼthupi lake pamene anamukhomerera pamtengo.+ Anachita zimenezi kuti tipulumutsidwe ku uchimo nʼkumachita zinthu zolungama. Ndipo “munachiritsidwa ndi mabala ake.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena