Aroma 12:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Musamatengere* nzeru za nthawi* ino, koma khalani munthu watsopano posintha kwambiri maganizo anu,+ kuti muzindikire chifuniro cha Mulungu,+ chabwino, chovomerezeka ndi changwiro. Aefeso 4:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndipo muvale umunthu watsopano+ umene unalengedwa mogwirizana ndi chifuniro cha Mulungu. Mukachita zimenezi mudzatha kuchita zimene zilidi zolungama ndi zokhulupirika.
2 Musamatengere* nzeru za nthawi* ino, koma khalani munthu watsopano posintha kwambiri maganizo anu,+ kuti muzindikire chifuniro cha Mulungu,+ chabwino, chovomerezeka ndi changwiro.
24 Ndipo muvale umunthu watsopano+ umene unalengedwa mogwirizana ndi chifuniro cha Mulungu. Mukachita zimenezi mudzatha kuchita zimene zilidi zolungama ndi zokhulupirika.