1 Atesalonika 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Munalandira mawuwo ndi chimwemwe chimene mzimu woyera+ umapereka ngakhale kuti munali pamavuto aakulu. Pamenepa munatsanzira ifeyo+ komanso munatsanzira Ambuye,+ 1 Atesalonika 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Chifukwa inu abale munatsanzira mipingo ya Mulungu yogwirizana ndi Khristu Yesu imene ili ku Yudeya. Tikutero chifukwa munayamba kuvutitsidwa ndi anthu akwanu,+ ngati mmene iwowonso akuvutitsidwira ndi Ayuda. 1 Petulo 2:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndipotu Mulungu anakuitanani kuti muyende mʼnjira imeneyi. Pajatu ngakhale Khristu anavutika chifukwa cha inu,+ ndipo anakusiyirani chitsanzo kuti mutsatire mapazi ake mosamala kwambiri.+
6 Munalandira mawuwo ndi chimwemwe chimene mzimu woyera+ umapereka ngakhale kuti munali pamavuto aakulu. Pamenepa munatsanzira ifeyo+ komanso munatsanzira Ambuye,+
14 Chifukwa inu abale munatsanzira mipingo ya Mulungu yogwirizana ndi Khristu Yesu imene ili ku Yudeya. Tikutero chifukwa munayamba kuvutitsidwa ndi anthu akwanu,+ ngati mmene iwowonso akuvutitsidwira ndi Ayuda.
21 Ndipotu Mulungu anakuitanani kuti muyende mʼnjira imeneyi. Pajatu ngakhale Khristu anavutika chifukwa cha inu,+ ndipo anakusiyirani chitsanzo kuti mutsatire mapazi ake mosamala kwambiri.+