Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 7:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Chenjerani ndi aneneri abodza+ amene amabwera kwa inu atavala ngati nkhosa,+ koma mkati mwa mitima yawo ali ngati mimbulu yolusa.+

  • Mateyu 7:22, 23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Pa tsiku limenelo ambiri adzandiuza kuti: ‘Ambuye, Ambuye,+ kodi ife sitinalosere mʼdzina lanu ndi kutulutsa ziwanda mʼdzina lanu ndiponso kuchita ntchito zambiri zamphamvu mʼdzina lanu?’+ 23 Koma ine ndidzawauza kuti: ‘Sindikukudziwani ngakhale pangʼono! Chokani pamaso panga, anthu osamvera malamulo inu.’+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena