1 Akorinto 9:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Munthu aliyense wochita nawo mpikisano amakhala wodziletsa pa zinthu zonse. Anthu amachita zimenezo kuti akalandire nkhata yakumutu imene imawonongeka,+ koma ife, kuti tikapeze nkhata yakumutu yomwe singawonongeke.+ Yakobo 1:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Wosangalala ndi munthu amene akupirira mayesero,+ chifukwa akadzavomerezedwa, adzalandira mphoto* ya moyo,+ imene Yehova* analonjeza onse amene akupitiriza kumukonda.+
25 Munthu aliyense wochita nawo mpikisano amakhala wodziletsa pa zinthu zonse. Anthu amachita zimenezo kuti akalandire nkhata yakumutu imene imawonongeka,+ koma ife, kuti tikapeze nkhata yakumutu yomwe singawonongeke.+
12 Wosangalala ndi munthu amene akupirira mayesero,+ chifukwa akadzavomerezedwa, adzalandira mphoto* ya moyo,+ imene Yehova* analonjeza onse amene akupitiriza kumukonda.+