Yakobo 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Tamverani abale anga okondedwa. Kodi Mulungu sanasankhe anthu amene dzikoli limawaona kuti ndi osauka kuti akhale olemera mʼchikhulupiriro+ komanso kuti akhale oyenera kupatsidwa Ufumu umene Mulungu analonjeza anthu amene amamukonda?+
5 Tamverani abale anga okondedwa. Kodi Mulungu sanasankhe anthu amene dzikoli limawaona kuti ndi osauka kuti akhale olemera mʼchikhulupiriro+ komanso kuti akhale oyenera kupatsidwa Ufumu umene Mulungu analonjeza anthu amene amamukonda?+