Ekisodo 1:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Iye anawauza kuti: “Mukamathandiza amayi a Chiheberi kubereka+ ndipo mwaona kuti mwana amene akubadwayo ndi wamwamuna muzimupha, koma ngati ndi wamkazi muzimusiya wamoyo.” Ekisodo 1:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kenako Farao analamula anthu ake onse kuti: “Mwana aliyense wamwamuna wobadwa kumene wa Aheberi muzimuponya mumtsinje wa Nailo, koma mwana aliyense wamkazi muzimusiya wamoyo.”+
16 Iye anawauza kuti: “Mukamathandiza amayi a Chiheberi kubereka+ ndipo mwaona kuti mwana amene akubadwayo ndi wamwamuna muzimupha, koma ngati ndi wamkazi muzimusiya wamoyo.”
22 Kenako Farao analamula anthu ake onse kuti: “Mwana aliyense wamwamuna wobadwa kumene wa Aheberi muzimuponya mumtsinje wa Nailo, koma mwana aliyense wamkazi muzimusiya wamoyo.”+