-
1 Mafumu 18:46Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
46 Koma dzanja la Yehova linapatsa Eliya mphamvu, moti anakokera chovala chake nʼkuchimanga mʼchiuno ndipo anayamba kuthamanga nʼkupitirira Ahabu mpaka kukafika ku Yezereeli.
-