-
Aefeso 1:20, 21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 pamene anazigwiritsa ntchito poukitsa Khristu kwa akufa nʼkumukhazika kudzanja lake lamanja+ mʼmalo akumwamba. 21 Anamuika pamwamba kuposa boma lililonse, ulamuliro uliwonse, anthu amphamvu onse, ambuye onse, ndi aliyense amene ali ndi dzina laulemu,+ osati mu nthawi* ino yokha, komanso imene ikubwerayo.
-