Levitiko 5:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Azibweretsanso kwa Yehova nsembe yake yakupalamula chifukwa cha tchimo limene wachita.+ Azibweretsa nkhosa yaingʼono yaikazi kapena mbuzi yaingʼono yaikazi kuti ikhale nsembe yamachimo. Akatero wansembe aziphimba tchimo la munthuyo.
6 Azibweretsanso kwa Yehova nsembe yake yakupalamula chifukwa cha tchimo limene wachita.+ Azibweretsa nkhosa yaingʼono yaikazi kapena mbuzi yaingʼono yaikazi kuti ikhale nsembe yamachimo. Akatero wansembe aziphimba tchimo la munthuyo.