Salimo 39:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Zoonadi, moyo wa munthu aliyense umangodutsa ngati chithunzithunzi. Iye amangovutika* popanda phindu. Amaunjika chuma, osadziwa kuti amene adzasangalale nacho ndi ndani.+ Miyambo 27:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Usadzitame ndi zimene udzachite mawaChifukwa sukudziwa zimene zidzachitike mawa.*+ Mlaliki 6:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndi ndani akudziwa zinthu zabwino zimene munthu angachite pa masiku ochepa a moyo wake wachabechabe, umene umakhala ngati mthunzi?+ Chifukwa ndi ndani angauze munthu zimene zidzachitike padziko lapansi pano iyeyo atafa?
6 Zoonadi, moyo wa munthu aliyense umangodutsa ngati chithunzithunzi. Iye amangovutika* popanda phindu. Amaunjika chuma, osadziwa kuti amene adzasangalale nacho ndi ndani.+
12 Ndi ndani akudziwa zinthu zabwino zimene munthu angachite pa masiku ochepa a moyo wake wachabechabe, umene umakhala ngati mthunzi?+ Chifukwa ndi ndani angauze munthu zimene zidzachitike padziko lapansi pano iyeyo atafa?