-
Luka 22:28-30Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
28 Komabe, inu ndi amene mwakhalabe ndi ine+ mʼmayesero anga.+ 29 Choncho ndikuchita nanu pangano, mofanana ndi mmene Atate wanga wachitira pangano la ufumu ndi ine,+ 30 kuti mukadye ndi kumwa patebulo langa mu Ufumu wanga,+ komanso kuti mukakhale mʼmipando yachifumu+ kuweruza mafuko 12 a Isiraeli.+
-