Machitidwe 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pa nthawi imeneyo, Ayuda oopa Mulungu ochokera mʼmitundu yonse yapadziko lapansi ankakhala ku Yerusalemu.+ Machitidwe 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pano pali Apati, Amedi+ ndi Aelamu.+ Palinso anthu ochokera ku Mesopotamiya, ku Yudeya, ku Kapadokiya, ku Ponto ndi kuchigawo cha Asia.+
5 Pa nthawi imeneyo, Ayuda oopa Mulungu ochokera mʼmitundu yonse yapadziko lapansi ankakhala ku Yerusalemu.+
9 Pano pali Apati, Amedi+ ndi Aelamu.+ Palinso anthu ochokera ku Mesopotamiya, ku Yudeya, ku Kapadokiya, ku Ponto ndi kuchigawo cha Asia.+