Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Machitidwe 23:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Paulo anayangʼanitsitsa Khoti Lalikulu la Ayudalo nʼkunena kuti: “Anthu inu, abale anga, ndachita zinthu popanda chikumbumtima changa kunditsutsa ngakhale pangʼono pamaso pa Mulungu+ mpaka lero.”

  • Machitidwe 24:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Chifukwa cha zimenezi, ndikuyesetsa mwakhama kuti ndikhale ndi chikumbumtima chabwino kwa Mulungu ndiponso kwa anthu.+

  • 1 Timoteyo 1:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Cholinga cha malangizo amenewa nʼchakuti tikhale ndi chikondi+ chochokera mumtima woyera, mʼchikumbumtima chabwino ndiponso mʼchikhulupiriro+ chopanda chinyengo.

  • 1 Timoteyo 1:18, 19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Mwana wanga Timoteyo, ndikukulangiza kuchita zimenezi mogwirizana ndi maulosi amene ananeneratu za iwe, kuti mogwirizana ndi maulosiwo upitirize kumenya nkhondo yabwino.+ 19 Ukhale ndi chikhulupiriro komanso chikumbumtima chabwino+ chimene anthu ena asiya kuchitsatira, moti chikhulupiriro chawo chasweka ngati ngalawa.

  • 1 Timoteyo 3:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Akhale ogwira chinsinsi chopatulika cha chikhulupiriro, ali ndi chikumbumtima choyera.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena