Aroma 6:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Nanunso muzidziona ngati akufa pa nkhani ya uchimo, koma amoyo kwa Mulungu mwa Khristu Yesu.+ Akolose 3:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Choncho chititsani ziwalo za thupi lanu+ padziko lapansi kukhala zakufa ku chiwerewere,* zinthu zodetsa, chilakolako chosalamulirika cha kugonana,+ kulakalaka zinthu zoipa komanso dyera limene ndi kulambira mafano. 1 Yohane 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Aliyense amene ali wogwirizana ndi Yesu sakhala ndi chizolowezi chochita tchimo.+ Amene ali ndi chizolowezi chochita tchimo ndiye kuti samukhulupirira* kapena kumudziwa.
5 Choncho chititsani ziwalo za thupi lanu+ padziko lapansi kukhala zakufa ku chiwerewere,* zinthu zodetsa, chilakolako chosalamulirika cha kugonana,+ kulakalaka zinthu zoipa komanso dyera limene ndi kulambira mafano.
6 Aliyense amene ali wogwirizana ndi Yesu sakhala ndi chizolowezi chochita tchimo.+ Amene ali ndi chizolowezi chochita tchimo ndiye kuti samukhulupirira* kapena kumudziwa.