Machitidwe 5:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Zitatero atumwiwo anachoka pamaso pa Khoti Lalikulu la Ayuda. Iwo anali osangalala+ chifukwa Mulungu anawaona kuti ndi oyenera kuchitiridwa chipongwe chifukwa cha dzina la Yesu. Yakobo 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Abale anga, muzisangalala kwambiri pamene mukukumana ndi mayesero osiyanasiyana,+
41 Zitatero atumwiwo anachoka pamaso pa Khoti Lalikulu la Ayuda. Iwo anali osangalala+ chifukwa Mulungu anawaona kuti ndi oyenera kuchitiridwa chipongwe chifukwa cha dzina la Yesu.