Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Aroma 8:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Choncho ngati tili ana, ndifenso olandira cholowa kuchokera kwa Mulungu. Koma ndifenso olandira cholowa+ anzake a Khristu, ngati tikuvutika naye limodzi+ kuti tikalandire naye ulemerero.+

  • 2 Akorinto 4:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Nthawi zonse timapirira tikamazunzidwa ngati mmene Yesu anachitira+ ndipo timachita zimenezi kuti moyo wa Yesu uonekerenso mwa ife.*

  • 2 Timoteyo 3:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Pajatu onse ofuna kukhala ndi moyo wodzipereka kwa Mulungu mogwirizana ndi Khristu Yesu, nawonso adzazunzidwa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena