Hoseya 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndipo Aisiraeli* adzachuluka ngati mchenga wakunyanja umene munthu sangathe kuuyeza kapena kuuwerenga.+ Ndipo kumene ankauzidwa kuti, ‘Siinu anthu anga,’+ adzauzidwa kuti, ‘Ndinu ana a Mulungu wamoyo.’+ Machitidwe 15:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Sumiyoni+ wafotokoza bwino mmene Mulungu anacheukira anthu a mitundu ina kwa nthawi yoyamba, kuti pakati pawo atengepo anthu odziwika ndi dzina lake.+ Aroma 9:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ndi zofanananso ndi zimene ananena mʼbuku la Hoseya kuti: “Anthu amene si anthu anga+ ndidzawatchula kuti ‘anthu anga,’ ndipo mkazi amene sankakondedwa ndidzamutchula kuti ‘wokondedwa.’+
10 Ndipo Aisiraeli* adzachuluka ngati mchenga wakunyanja umene munthu sangathe kuuyeza kapena kuuwerenga.+ Ndipo kumene ankauzidwa kuti, ‘Siinu anthu anga,’+ adzauzidwa kuti, ‘Ndinu ana a Mulungu wamoyo.’+
14 Sumiyoni+ wafotokoza bwino mmene Mulungu anacheukira anthu a mitundu ina kwa nthawi yoyamba, kuti pakati pawo atengepo anthu odziwika ndi dzina lake.+
25 Ndi zofanananso ndi zimene ananena mʼbuku la Hoseya kuti: “Anthu amene si anthu anga+ ndidzawatchula kuti ‘anthu anga,’ ndipo mkazi amene sankakondedwa ndidzamutchula kuti ‘wokondedwa.’+