Aroma 13:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Choncho pali chifukwa chabwino choti muzigonjera, osati chabe chifukwa choopa mkwiyowu koma chifukwanso cha chikumbumtima chanu.+
5 Choncho pali chifukwa chabwino choti muzigonjera, osati chabe chifukwa choopa mkwiyowu koma chifukwanso cha chikumbumtima chanu.+