1 Petulo 2:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ngati munthu akupirira pamene akuzunzidwa komanso kukumana ndi mavuto* chifukwa chomvera* Mulungu,+ Mulunguyo amasangalala naye. 1 Petulo 3:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Muzikhala ndi chikumbumtima chabwino,+ kuti kaya anthu akunenereni zoipa, amene akukunenerani zoipawo adzachite manyazi+ chifukwa cha khalidwe lanu labwino monga otsatira a Khristu.+
19 Ngati munthu akupirira pamene akuzunzidwa komanso kukumana ndi mavuto* chifukwa chomvera* Mulungu,+ Mulunguyo amasangalala naye.
16 Muzikhala ndi chikumbumtima chabwino,+ kuti kaya anthu akunenereni zoipa, amene akukunenerani zoipawo adzachite manyazi+ chifukwa cha khalidwe lanu labwino monga otsatira a Khristu.+