Yohane 13:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Chifukwa ndakupatsani chitsanzo kuti mmene ine ndachitira kwa inu, inunso muzichita chimodzimodzi.+ Aroma 16:3, 4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mundiperekere moni kwa Purisika ndi Akula,+ antchito anzanga potumikira Khristu Yesu. 4 Iwo anaika miyoyo yawo pachiswe chifukwa cha ine,+ ndipo si ine ndekha amene ndikuwayamikira, komanso mipingo yonse ya anthu a mitundu ina. 1 Atesalonika 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Choncho popeza timakukondani kwambiri,+ tinkafunitsitsa* kukuuzani uthenga wabwino wa Mulungu komanso kupereka miyoyo yathu yeniyeniyo+ kuti tikuthandizeni.
15 Chifukwa ndakupatsani chitsanzo kuti mmene ine ndachitira kwa inu, inunso muzichita chimodzimodzi.+
3 Mundiperekere moni kwa Purisika ndi Akula,+ antchito anzanga potumikira Khristu Yesu. 4 Iwo anaika miyoyo yawo pachiswe chifukwa cha ine,+ ndipo si ine ndekha amene ndikuwayamikira, komanso mipingo yonse ya anthu a mitundu ina.
8 Choncho popeza timakukondani kwambiri,+ tinkafunitsitsa* kukuuzani uthenga wabwino wa Mulungu komanso kupereka miyoyo yathu yeniyeniyo+ kuti tikuthandizeni.