Numeri 16:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Choncho iwo anasonkhana nʼkuyamba kutsutsana+ ndi Mose ndi Aroni kuti: “Tatopa nanu tsopano. Gulu lonseli ndi loyera,+ ndipo Yehova ali pakati pawo.+ Nanga nʼchifukwa chiyani inu mukudzikweza pa mpingo wa Yehova?” Numeri 16:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Nthakayo inangʼambika* nʼkuwameza limodzi ndi mabanja awo komanso anthu ena onse amene anali kumbali ya Kora+ pamodzi ndi katundu wawo yense.
3 Choncho iwo anasonkhana nʼkuyamba kutsutsana+ ndi Mose ndi Aroni kuti: “Tatopa nanu tsopano. Gulu lonseli ndi loyera,+ ndipo Yehova ali pakati pawo.+ Nanga nʼchifukwa chiyani inu mukudzikweza pa mpingo wa Yehova?”
32 Nthakayo inangʼambika* nʼkuwameza limodzi ndi mabanja awo komanso anthu ena onse amene anali kumbali ya Kora+ pamodzi ndi katundu wawo yense.