Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Aheberi 6:4-6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Pali anthu amene Mulungu anawaunikira,+ amene analandirapo mphatso yaulere yakumwamba, amene analandira mzimu woyera 5 komanso amene anamvapo mawu abwino a Mulungu ndi madalitso* amene adzaperekedwe padziko limene likubweralo. 6 Koma tsopano anthu amenewa anagwa+ ndipo nʼzosatheka kuwadzutsanso kuti alape, chifukwa akupachika kachiwiri Mwana wa Mulungu ndiponso kumunyoza poyera.+

  • Chivumbulutso 21:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Koma anthu amantha, opanda chikhulupiriro,+ odetsedwa amenenso amachita zinthu zonyansa, opha anthu,+ achiwerewere,*+ amene amachita zamizimu, olambira mafano ndi anthu onse abodza,+ adzaponyedwa mʼnyanja yoyaka moto ndi sulufule.+ Nyanja imeneyi ikuimira imfa yachiwiri.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena