Ekisodo 30:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “Upange beseni losambira lakopa+ ndi choikapo chake. Ukatero uliike pakati pa chihema chokumanako ndi guwa lansembe ndipo uthiremo madzi.+ 1 Mafumu 7:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Kenako iye anapanga thanki yosungira madzi.*+ Thankiyo inali yozungulira ndipo inali mikono 10 kuchokera mbali ina kufika ina, kuyeza modutsa pakati. Thankiyo inali yaitali mikono 5 ndipo kuzungulira thanki yonseyo inali mikono 30.+
18 “Upange beseni losambira lakopa+ ndi choikapo chake. Ukatero uliike pakati pa chihema chokumanako ndi guwa lansembe ndipo uthiremo madzi.+
23 Kenako iye anapanga thanki yosungira madzi.*+ Thankiyo inali yozungulira ndipo inali mikono 10 kuchokera mbali ina kufika ina, kuyeza modutsa pakati. Thankiyo inali yaitali mikono 5 ndipo kuzungulira thanki yonseyo inali mikono 30.+