Mateyu 24:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Chifukwa pa nthawiyo kudzakhala chisautso chachikulu+ chimene sichinachitikepo kuchokera pachiyambi cha dziko mpaka lero, ndipo sichidzachitikanso.+ Maliko 13:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Chifukwa masiku amenewo adzakhala masiku a chisautso+ chimene sichinachitikepo kuchokera pachiyambi cha chilengedwe chimene Mulungu analenga kudzafika nthawi imeneyo ndipo sichidzachitikanso.+
21 Chifukwa pa nthawiyo kudzakhala chisautso chachikulu+ chimene sichinachitikepo kuchokera pachiyambi cha dziko mpaka lero, ndipo sichidzachitikanso.+
19 Chifukwa masiku amenewo adzakhala masiku a chisautso+ chimene sichinachitikepo kuchokera pachiyambi cha chilengedwe chimene Mulungu analenga kudzafika nthawi imeneyo ndipo sichidzachitikanso.+