Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Danieli 12:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 “Pa nthawi imeneyo Mikayeli,*+ kalonga wamkulu+ amene waimirira kuti athandize anthu a mtundu wako,* adzaimirira. Ndiyeno padzafika nthawi yamasautso imene sinakhalepo kuyambira pamene mtundu woyambirira wa anthu unakhalapo kudzafika nthawi imeneyo. Pa nthawi imeneyo anthu a mtundu wako, aliyense amene dzina lake lidzakhala litalembedwa mʼbuku, adzapulumuka.+

  • Afilipi 4:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Ndikupempha iwenso wantchito mnzanga weniweni,* kuti upitirize kuwathandiza azimayi amenewa. Iwo ayesetsa mwakhama kugwira ntchito yolengeza uthenga wabwino limodzi ndi ine. Achita zimenezi limodzinso ndi Kilementi komanso antchito anzanga ena onse amene mayina awo ali mʼbuku la moyo.+

  • Chivumbulutso 13:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Anthu amene akukhala padziko lapansi adzachilambira. Kuchokera pamene dziko linakhazikitsidwa, anthu amenewa mayina awo sanalembedwe mumpukutu wa moyo+ wa Mwanawankhosa amene anaphedwa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena