MIKA
ZIMENE ZILI MʼBUKULI
1
2
3
4
5
Wolamulira amene adzakhale wamphamvu padziko lonse (1-6)
Anthu otsala adzakhala ngati mame komanso mkango (7-9)
Dziko lidzayeretsedwa (10-15)
6
Mulungu anaimba mlandu Aisiraeli (1-5)
Yehova akufuna kuti uzichita chiyani? (6-8)
Aisiraeli analakwa nʼkulangidwa (9-16)
7
Makhalidwe oipa a Aisiraeli (1-6)
“Ine ndidzayembekezera Yehova” (7)
Anthu a Mulungu zinthu zidzawayendera bwino (8-13)
Mika anapemphera komanso kutamanda Mulungu (14-20)