Tsamba 2
Kutchova Juga Kodi Kumafupa? 3-11
Kuzungulira dziko lonse lapansi anthu mamiliyoni ambiri amayesa mwaŵi wawo mwakuseŵera lotale ndi mitundu ina ya kutchova juga. Kumakhala kovuta kwa ambiri kukaniza chikhumbo cha chuma chopezeka mwamsanga, makamaka osauka. Koma kodi kutchova juga ndiko njira yabwino yopezera chuma? Kodi pali njira yabwinopo?
Kodi Ndiyenera Kukhaliranji Wosiyana? 18
Akristu achichepere ali osiyana ndi achichepere ena m’njira zambiri. Kodi nchifukwa ninji? Kodi ndani amapindula?