Tsamba 2
Chisudzulo—Kodi Chili Njira Yomkira ku Moyo Wachimwemwe Kwambiri? 3-11
Chisudzulo chikukhala njira yovomerezeka yopezera moyo wachimwemwe kwambiri. Kumaiko a Kum’maŵa nakonso, kumene kalelo chisudzulo sichinali kuvomerezedwa, chiŵerengero chikuwonjezereka. Kodi chisudzulo ndicho njira yokha yotulukira muukwati wopanda chimwemwe?
Kodi Kulota Uli Maso Nkolakwa? 16
Kulota uli maso nkofala pakati pa achichepere ndi achikulire; komabe, kodi nkovulaza?
[Mawu a Chithunzi patsamba 2]
Scala/Art Resource, N.Y.