Tsamba 2
Kodi Mafuko Onse Adzagwirizana Konse? 3-11
Kodi nchifukwa ninji kusankhana ndi kutsenderezana kwa mafuko kuli kofala kwambiri? Kodi kusiyana kwa khungu pakati pa mafuko kumatanthauza kuti ali osiyana kotheratu? Kodi anthu a mafuko osiyana angakhale limodzi mu mtendere?
Kodi Ndimotani Mmene Ndingapeŵere Kutenga AIDS? 23
AIDS tsopano ili pakati pa matenda opatsirana mwakugonana amene akukantha achichepere kuzungulira dziko lonse. Kodi chinthu chothandiza kwambiri kutchinjiriza kufalikira kwa AIDS nchiyani?