Tsamba 2
KANSA YA MAŴERE—Nkhaŵa ya Mkazi Aliyense 3-10
Kansa ya maŵere imakantha akazi zikwi mazana ambiri chaka chilichonse. Kodi nchiyani chimene chimaichititsa? Kodi ingapeŵedwe kapena kuchiritsidwa?
Kodi Nthaŵi Zonse Kumakhala Kulakwa Kukwiya? 27
Kodi pali nthaŵi zina pamene mkwiyo sumalungamitsidwa chabe koma umakhala woyenera?
Kodi Kudzipha Ndiko Yankho? 29
Kodi achichepere angathandizidwe motani kuzindikira kuti kudzipha sikuli yankho la mavuto a moyo?