Tsamba 2
Chuma Chakuthupi Kodi Ndicho Mfungulo Yopezera Dziko Lachimwemwe? 3-9
Kodi chuma chakuthupi ndicho yankho la mavuto a dziko? Ngati sichili, kodi yankho lake nchiyani?
Kodi Ndinu Womvetsera Wachifundo? 10
Mmene mungakhalire womvetsera kwambiri pamene ena akulankhula nanu.
Kodi Mulungu Amapereka Mphotho? 30
Pamene anthu achita chifuniro cha Mulungu, kodi angayembekezere mphotho?