Tsamba 2
Maunyolo ndi Misozi ya Ukapolo 3-8
Ukapolo unakhudza miyoyo ya amuna, akazi, ndi ana mamiliyoni ambiri a mu Afirika. Kodi chinawachitikira nchiyani? Kodi unali mlandu wa yani?
Kukhululukira ndi Kuiŵala—Kodi Nkotheka Motani? 9
Pamene munthu wina wakulakwirani kwambiri, kodi mukhoza kumkhululukira ndi kuiŵala? Kodi muyenera kutero?