Zisonyezero za Voliyumu 76 ya Galamukani!
ACHICHEPERE AKUFUNSA KUTI
Kuba—Kulekeranji?, 7/8
Kukhala Bwenzi la Mulungu, 8/8, 12/8
Kukonza Moyo, 1/8
Kuloŵa Msanga mu Ukwati, 5/8
Kupeza Zovala Zoyenera, 2/8
Kutaya Mimba Ndiko Yankho?, 3/8
Kuvutitsidwa ndi Amuna Kapena Akazi, 9/8
Makolo Ochita Molakwa, 6/8
Nchifukwa Ninji Aliyense Akuloŵa mu Ukwati?, 11/8
Ndiphunzire Kudzitetezera?, 10/8
Umathanyula, 2/8, 3/8, 4/8
CHIPEMBEDZO
Bungwe la World Council of Churches, 4/8
Chimene Matchalitchi Anakhalira Chete, 9/8
Kodi Adzalalikira Khomo ndi Khomo?, 3/8
Kodi Siali a Dziko Lapansi?, 1/8
Kufunafuna Waluso Wamkulu Koposa, 11/8
Mabishopu a Italy Akuda Nkhaŵa, 3/8
Krisimasi—Chiyambi Chake, 12/8
Mapeto a Dziko, 7/8
Tchalitchi cha Katolika mu Afirika, 1/8
CHUMA NDI NTCHITO YOLEMBEDWA
Chipululutso cha Zachuma, 5/8
Kuloŵa m’Ngongole Kumathandiza?, 6/8
LINGALIRO LA BAIBULO
Chifuno cha Moyo, 5/8
Chigololo—Kukhululukira Kapena Kusakhululukira?, 8/8
Kodi Mpikisano m’Maseŵero Ngwoipa?, 12/8
Kodi Zimene Mumakhulupirira Zili Nkanthu?, 7/8
Kukhululukira ndi Kuiŵala—Kodi Nkotheka Motani?, 6/8
Mbali Yanu m’Mapemphero Anu, 9/8
Miyezo ya Mulungu ndi Yosafikirika?, 10/8
Mulungu Amakondwa Kutiona Tikuvutika?, 3/8
Ndani Amapita Kumwamba?, 1/8
Umbeta, 2/8
MAIKO NDI ANTHU
Kuchokera ku Mabotolo Kukhala Mkanda (Nigeria), 11/8
Kumene Ziombankhanga Zimaulukira Kukadya Nsomba (Alaska), 12/8
Sukulu ya mu Afirika, 10/8
Tanthauzo la Nyawu (Afirika), 8/8
MAUNANSI A ANTHU
Ana Osoŵa, 2/8
Kodi Mumaŵerengera Agogo?, 7/8
Mabanja a Kholo Limodzi, 10/8
MBONI ZA YEHOVA
Chimene Analankhulira Mopanda Mantha, 9/8
Chipolopolo Chinasintha Moyo Wanga (G. Williams), 11/8
Kumene Ndalama Zimakhala m’Mitengo, 7/8
Kupanga Ophunzira Enieni Lerolino, 1/8
Kusamalira Ovutika ndi Tsoka la ku Rwanda, 1/8
Lingaliro Langa la Ntchito ya Madokotala Lasintha, 2/8
Liwu Lomvekapo Lokha Kuli Chete?, 9/8
Mabuku Ayamikiridwa m’Maiko Amene Anali Soviet Union, 6/8
Ulendo Wobwereza ku Russia, 3/8
Zaka Zoposa 40 Pansi pa Chiletso cha Komyunizimu (J. Hálová), 5/8
SAYANSI
Iceman, 5/8
Miyala Imene Imauluka, 12/8
UMOYO NDI MANKHWALA
Chakudya Chanu Chilidi Chomanga Thupi?, 3/8
Fungo Loipa la m’Kamwa, 7/8
Khungu la mu Mtsinje, 10/8
Kudwala kwa Mkazi Ali Pafupi Kusamba, 8/8
Kumene AIDS Uli Mliri Waukulu, 8/8
Kupsa ndi Ntchito, 1/8
Kusiyana m’Zathanzi kwa Padziko Lonse, 4/8
Miyoyo Mamiliyoni Ambiri Ikuthera mu Utsi (Kusuta), 6/8
Nchifukwa Ninji Moyo Uli Waufupi Motere?, 11/8
Nthenda za m’Chakudya, 12/8
Nyengo Yoleka Kusamba, 3/8
Pamene Sikudzakhalanso Matenda, 4/8
ZINYAMA NDI ZOMERA
Chipembere, 8/8
Chiswe—Bwenzi Kapena Mdani?, 6/8
“Mtengo wa Moyo” Wodabwitsa wa Afirika (Mulambe), 4/8
Ng’ona, 4/8
Njati ya m’Madzi—Yokhulupirika ndi Yothandiza, 8/8
Nyalugwe, 4/8
ZOCHITIKA ZA DZIKO NDI MIKHALIDWE YAKE
Ana Osoŵa, 2/8
Chakudya Chokwanira kwa Onse! 11/8
Juga—Kumwerekera Komakula, 10/8
Kodi Ano Ndiwo Masiku Otsiriza?, 5/8
Kodi Maiko Olemera Adzadyerera Osauka Nthaŵi Zonse?, 12/8
Kodi Munthu Adzakhoza Kulimbana ndi Masoka?, 8/8
Kusiyana m’Zathanzi kwa Padziko Lonse, 4/8
Kuvumbula Zoipa za Nazi?, 9/8
Maiko Osauka Akhala Kotayira Zinyalala, 12/8
Maunyolo ndi Misozi ya Ukapolo, 6/8
1945-1995, 9/8
ZOSIYANASIYANA
Kunyong’onyeka, 2/8
Kuzengereza—Mbala ya Nthaŵi, 4/8
Njira ya Mwana Yoyendera, 12/8
Mpunga—Wophika Kapena Wosaphika?, 2/8
[Bokosi patsamba 32]
Ngati mungafune chidziŵitso chowonjezereka kapena phunziro la Baibulo la panyumba laulere, chonde lemberani Watch Tower kapena kukeyala yoyenera pandandanda ya patsamba 5.