Tsamba 2
Pamene Sikudzakhalanso Nkhondo 3-11
Ziyembekezo za mtendere wa dziko zikuonekera kukhala zosatsimikizirika. Ngakhale kuti ambiri akuyembekezera zoipa, kodi nchifukwa ninji tingathe kukhala achidaliro chakuti dziko lopanda nkhondo layandikira?
AIDS mu Afirika—Kodi Dziko Lachikristu Lili ndi Mlandu Waukulu Motani? 12
AIDS yasakaza Afirika kwambiri. Kodi matchalitchi ali ndi thayo lotani pa zimenezi?
[Mawu a Chithunzi patsamba 2]
Chikuto chakutsogolo pamwamba: Chithunzi cha U.S. National Archives.
Chikuto chakutsogolo pamwamba kulamanja: Chithunzi cha WHO chojambulidwa ndi W. Cutting.
Chikuto chakumbuyo pamwamba kulamanja: Chithunzi cha USAF.