Tsamba 2
Vuto La Othaŵa Kwawo—kodi Lidzathadi? 3-11
Anthu mamiliyoni makumi ambiri akakamizidwa kuthaŵa. Kodi moyo ngwotani kwa othaŵa kwawo? Kodi nchifukwa ninji vutolo likuipiraipirabe? Kodi chothetsera chake nchiyani?
Kodi Ndiyenera Kuchita Maseŵero Apakompyuta Kapena Apavidiyo? 12
Maseŵero apakompyuta ndi apavidiyo amaoneka ngati zosangulutsa zabwino. Kodi mukudziŵa kuipa kwake? Kodi mudzasankha mwanzeru?
[Mawu a Chithunzi patsamba 2]
Chikuto: Albert Facelly/Sipa Press
Logo for pages 16, 19, and 24: Indian face: D. F. Barry Photograph, Thomas M. Heski Collection; dancing Indian: Men: A Pictorial Archive from Nineteenth-Century Sources/Dover Publications, Inc.; tepees: Leslie’s; rectangular design: Decorative Art; circular designs: Authentic Indian Designs