Tsamba 2
Kupirira Nsautso ya Stroko 3-12
Chimapangitsa Stroko Nchiyani? Kodi Munthu Angapirire Motani Zotsatira Zake?
Kodi Umodzi Wachikristu Umalola Maumunthu Osiyanasiyana? 13
Kodi kusiyana maumunthu tingakulolere mpaka pati?
Momwe Ndimakhalira Monga Wachibwibwi 16
Wachibwibwi akunena mavuto amene wakhala akukumana nawo kuyambira paubwana wake.