Za M’katimu
TSAMBA MUTU
5 1 Muli ndi Chifukwa Chokhalira Odera Nkhawa
9 2 M’mene Imfa Imayambukirira Zochita za Tsiku ndi Tsiku za Anthu
16 3 Munthu Anapangidwa Kukhala ndi Moyo
26 4 Kodi Ukalamba ndi Imfa Zinakhalako Motani?
355 Kodi Chinthu Ichi Chochedwa “Moyo” n’Chiani?
476 Mzimu Umene Umabwerera kwa Mulungu
607 Kodi Akufa Amafuna Chithandizo Chanu?
698 Kodi Muyenera Kuopa Akufa?
749 odi Mungathe Kulankhula ndi Akufa?
7810 Kodi Chingakhale Chinyengo Chochenjera?
11013 Bwanji Ponena za Moto wa Gehena?
11714 Chimene ‘Chizunzo m’Nyanja ya Moto’ Chimatanthauza
12515 Boma Limene Lidzagonjetsa Mdani wa Munthu Imfa
13316 Dziko Lapansi Lopanda Matenda ndi Imfa
14317 Chimene Moyo Wosatha pa Dziko Lapansi Umatipatsa
15118 Chifukwa Chake Ambiri Amene Ali ndi Moyo Tsopano Ali ndi Mwai wa Kusafa Konse
16619 Mabiliyoni Amene Ali Akufa Tsopano Adzakhala’nso ndi Moyo Posachedwa
17620 Kodi Chiukiriro Chidzadzetsa Mapindu Yani?
18621 Kodi Ndi Motani M’mene Mungakhalire ndi Moyo Woposa Uno?
TAMVERANI: Kusiyapo ngati kutasonyezedwa mwa njira ina, mau a Baibulo ogwidwa m’bukhu lino ali ochokera mu Revised Union Nyanja Version. Malemba olembedwamo osonyezedwa ndi chizindikiro cha NW ndi MO amasonyeza kumene chidziwitso chimodzi-modzi’cho chikupezeka mu New World Translation of the Holy Scriptures m’Chingelezi ndi Malembo Oyera, Baibulo Lachikatolika.