Za M’katimu
TSAMBA MUTU
5 1 Ulamuliro Wotsatirapo wa Dziko Lonse Lapansi
17 2 Wolamulira Amene Amadziwa Mapeto Kuyambira Pachiyambi
37 3 Masinthidwe a Dziko Onenedweratu Kufikira ku Ufumu wa Mulungu
64 4 M’mene Ufumu wa Mulungu Ukukhalira Boma la Dziko
71 5 Kuneneratu Nthawi ya Ulamuliro wa Dziko
90 6 Woimira Wamkulu wa Mulungu m’Boma la Dziko
108 7 Kusankha Okhala ndi Phande mu Ulamuliro wa Dziko
121 8 Masiku Osonyezedwa M’kati mwa “Nthawi ya Mapeto”
148 9 Chizindikiro” cha Kuyandikira kwa Boma la Dziko
160 10 “Khamu Lalikulu” Litamanda Boma la Dziko Likudza’lo
175 11 Kupita kwa Dziko Logawanika
183 12 M’mene Tingasangalalire ndi Boma la Dziko Kosatha
Kusiyapo ngati kwasonyezedwa mwa njira ina, kugwira malemba konse ndi kuchulidwa kopangidwa m’bukhu lino kwachokera m’Baibulo la Revised Union Nyanja Version, NW akumakhala chidule cha New World Translation of the Holy Scriptures, kusindikiza kwa 1971.
Ponena za madeti, chidule’cho B.C.E., chimaimira “Nyengo Ino Isanakhale,” ndipo C.E. amaimira “Za Nyengo Ino.”