Za Mkatimu
TSAMBA MUTU
5 1 Mtendere Weniweni ndi Chisungiko Zayandikira!
10 2 Kodi Anthu Angadzetse Mtendere Wosatha ndi Chisungiko?
22 3 Kodi Zipembedzo za Dziko Zikupereka Chitsogozo Choyenera?
34 4 Chiwonongeko cha Dziko Lonse Choyamba—Kenako Mtendere wa Dziko Lonse
43 5 Nkhani Imene Ikulowetsamo Inu
55 6 Kodi Mulungu Wakhala Akuchitanji?
69 7 Kodi Chiwonongeko cha Dziko Chonenedweratucho Chidzadza Liti?
86 8 Kodi Ndani Amene Adzakhala Opulumuka?
94 9 Mtendere ndi Chisungiko pa Dziko Lonse Lapansi—Chiyembekezo Chodalirika
108 10 Kodi Mukufunitsitsa Kuyang’anizana ndi Chowonadi m’Moyo Wanu?
117 11 Opulumuka Sayenera Kukhala “Mbali ya Dziko”
129 12 Kulemekeza Ulamuliro Nkofunika kaamba ka Moyo Wamtendere
142 13 Lingaliro Lanu la Kugonana—Kodi Limapanga Kusiyana Kotani?
152 14 Kulemekeza Mphatso ya Moyo
163 15 Kodi Nchifukwa Ninji Kudera Nkhaŵa ndi Anthu Ena?
175 16 Chosankha Chotsimikiziritsa Moyo mu Mtendere Weniweni ndi Chisungiko
187 Maumboni
Malemba otchulidwa m’bukhu lino angapezedwe m’matembenuzidwe ali onse a Baibulo. Komabe, kusiyapo ngati kwasonyezedwa mwa njira ina, mawu ogwidwa mwachindunji ali ochokera mu Revised Union Nyanja Version. Zondandalikidwa pansipa ndizo zidule za maina a matembenuzidwe ena a Baibulo ogwidwa mawu:
NE — The New English Bible (1970).
Ro — The Emphasized Bible (1897), Joseph B. Rotherham.
NW — New World Translation of the Holy Scriptures.