Mutu wa Buku Lino/Tsamba la Ofalitsa
Pindulani ndi Sukulu ya Utumiki wa Mulungu
“Ine ndine Yehova, Mulungu wako, amene ndikuphunzitsa kupindula, amene ndikutsogolera m’njira yoyenera iwe kupitamo.”—Yes. 48:17.
© 2002
WATCH TOWER BIBLE AND TRACT SOCIETY OF PENNSYLVANIA
Ulamuliro wonse pa buku lino n’ngwathu
Ofalitsa
PRINTED BY WATCH TOWER BIBLE AND TRACT SOCIETY OF SOUTH AFRICA NPC
1 Robert Broom Drive East, Range view, Krugersdorp, 1739, RSA.
Linasindikizidwa mu Losindikizidwa mu December 2014
Bukuli sitigulitsa. Timalipereka ngati njira imodzi yophunzitsa anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo.
Malemba m’buku lino akuchokera m’Baibulo la Revised Nyanja (Union) Version, kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina. Komabe, Chinyanjacho tachilemba m’kalembedwe katsopano. Pamene tasonyeza NW, ndiye kuti lembalo lachokera m’Baibulo la New World Translation of the Holy Scriptures—With References.