Zam’katimu
Tsamba
5 Takulandirani ku Sukulu ya Utumiki wa Mulungu
9 Kondwerani ndi Mawu a Mulungu
13 “Yang’anirani Mamvedwe Anu”
17 Mukhoza Kunola Luso Lanu Lokumbukira Zinthu
43 Kukonzekera Nkhani ya Wophunzira mu Sukulu
47 Kukonzekera Nkhani Zokambira Mpingo
56 Kulitsani Luso la Kuphunzitsa
62 Mmene Mungakulitsire Luso la Kucheza ndi Anthu
66 Dziŵani Mayankhidwe Oyenera
74 Khalani Womapitabe Patsogolo
78 Pulogalamu Yophunzitsa Luso la Kulankhula ndi Kuphunzitsa
82 Gwiritsani Ntchito Mitundu Yosiyanasiyana ya Makambirano
Mmene Mungapitire Patsogolo
Tsamba Phunziro
101 6 Kutsindika Ganizo Moyenerera
105 7 Kutsindika Malingaliro Ofunika Kwambiri
107 8 Mphamvu ya Mawu Yoyenerera
118 11 Mzimu Waubwenzi ndi Mmene Mukumvera
121 12 Manja ndi Nkhope Polankhula
131 15 Kuoneka Bwino
135 16 Kudekha
139 17 Kugwiritsa Ntchito Maikolofoni
143 18 Kugwiritsa Ntchito Baibulo Popereka Mayankho
145 19 Kulimbikitsa Omvera Kuŵerenga Baibulo
147 20 Kutchula Malemba Moyenerera
150 21 Kutsindika Malemba Moyenerera
153 22 Kugwiritsa Ntchito Malemba Moyenerera
157 23 Kumveketsa Phindu la Nkhani Yanu
166 25 Kugwiritsa Ntchito Autilaini
170 26 Kukamba Nkhani M’njira Yotsatirika
174 27 Kulankhula Kuchokera mu Mtima
179 28 Kukamba Nkhani Mmene Mumalankhulira ndi Anthu
181 29 Kamvekedwe Kabwino ka Mawu
186 30 Kusonyeza Chidwi mwa Munthu Winayo
197 33 Khalani Wosamala Komanso Wolimba
206 35 Kubwereza Komveketsa Mfundo
209 36 Kutambasula Mutu wa Nkhani
212 37 Kuunika Mfundo Zazikulu
215 38 Mawu Oyamba Okopa Chidwi
220 39 Mawu Omaliza Ogwira Mtima
223 40 Kunena Zoona Zokhazokha
226 41 Lankhulani Zomveka Bwino kwa Ena
230 42 Nkhani Yophunzitsadi Kanthu Omvera
234 43 Kukamba Mfundo za M’nkhani Imene Mwapatsidwa
236 44 Kugwiritsa Ntchito Mafunso Mwaluso
240 45 Mafanizo ndi Zitsanzo Zophunzitsadi
244 46 Mafanizo a Zinthu Zodziŵika Bwino
247 47 Kugwiritsa Ntchito Mwaluso Zinthu Zooneka Pophunzitsa
255 49 Kupereka Zifukwa Zomveka
258 50 Yesetsani Kuwafika Pamtima Anthu
263 51 Kusunga Nthaŵi ndi Kuigaŵa Bwino
265 52 Kulimbikitsa Ena Mogwira Mtima Kuti Achitepo Kanthu
268 53 Kulimbikitsa Omvera ndi Kuwatsitsimutsa
272 Uthenga Umene Tiyenera Kulengeza
282 Malangizo kwa Oyang’anira Sukulu
286 Mlozera Nkhani