Mutu wa Buku Lino/Tsamba la Ofalitsa
Kodi Mungatani Kuti ‘Mulungu Apitirize Kukukondani’?
Photo Credits:
◼ Page 14: © COMSTOCK Images/age fotostock
◼ Page 134: Mixa/age fotostock
◼ Page 201: © bilderlounge/Tips RF/age fotostock
Bukuli sitigulitsa. Timapereka ngati njira imodzi yophunzitsa anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo.
Ngati mukufuna kupereka, pitani pawebusaiti yathu ya www.pr2711.com/ny.
Malemba onse m’buku lino akuchokera m’Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina.
Losindikizidwa mu August 2017
Chichewa (lv-CN)
© 2009, 2014
Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania