Mutu wa Buku Lino/Tsamba la Ofalitsa
Zimene tingaphunzire munkhani za m’Baibulo
Bukuli sitigulitsa. Timalipereka ngati njira imodzi yophunzitsira anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo.
Ngati mukufuna kupereka, pitani pawebusaiti yathu ya donate.jw.org.
Malemba onse m’bukuli akuchokera mu Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, lolembedwa m’Chichewa chamakono, kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina.
Losindikizidwa mu November 2024
Chichewa (lfb-CN)
© 2017, 2024
Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania