Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • lfb tsamba 12-13
  • Mawu Oyamba Gawo 2

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Mawu Oyamba Gawo 2
  • Zimene Tingaphunzire Munkhani za M’Baibulo
  • Nkhani Yofanana
  • Kodi Chabwino Chidzagonjetsadi Choipa?
    Nsanja ya Olonda—1993
  • Mmene Chabwino Chidzagonjetsere Choipa
    Nsanja ya Olonda—2006
  • Chigumula Chisanachitike, Kodi Ndani Anamvera Mulungu Ndipo Ndani Amene Sanamumvere?
    Mverani Mulungu Kuti Mudzapeze Moyo Wosatha
  • Kutengerapo Chenjezo pa Zochitika Zakale
    Mungathe Kukhala Bwenzi la Mulungu!
Onani Zambiri
Zimene Tingaphunzire Munkhani za M’Baibulo
lfb tsamba 12-13
Nowa akulowetsa zinyama m’chingalawa

Mawu Oyamba Gawo 2

N’chifukwa chiyani Yehova anabweretsa chigumula chimene chinawononga zamoyo zonse? Kale kwambiri anthu asanachuluke padzikoli, Satana anachititsa kuti anthu asamamvere Yehova. Anthu ena monga Adamu, Hava ndi mwana wawo Kaini anasankha kuchita zofuna za Satana. Koma panalinso anthu ena ochepa monga Abele ndi Nowa omwe anasankha kuchita zimene Yehova amafuna. Pofika nthawi ya Nowa anthu ambiri ankachita zoipa, n’chifukwa chake Yehova anawononga dziko loipalo. Chigawochi chitithandiza kudziwa kuti Yehova amaona ngati tasankha kukhala kumbali yake kapena kukhala kumbali ya Satana, ndipo sadzalola kuti Satana alepheretse zolinga zake.

ZIMENE TIPHUNZIRE M’CHIGAWOCHI

  • Tiyenera kukhala anthu amtendere osati achiwawa ngati Satana ndi otsatira ake

  • Tikamamvera Mulungu ngati mmene Nowa anachitira, tidzakhala osangalala komanso tidzapeza moyo wosatha

  • Yehova amaona zonse zimene anthu akuchita. Ndipo amasangalala ndi anthu amene amachita zabwino koma amakwiya ndi anthu ochita zoipa

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena