Kodi Mungakonde Kuchezeredwa?
Ngakhale m’dziko lino lodzala ndi mavuto, mungakhoze kupeza chimwemwe kuchokera m’chidziŵitso cholongosoka cha Baibulo chonena za Mulungu, Ufumu wake, ndi chifuno chake chabwino kwambiri kwa anthu. Ngati mungafune chidziŵitso chowonjezereka kapena ngati mungakonde kuti wina adze kudzachita nanu phunziro Labaibulo lapanyumba laulere, chonde lemberani ku Watch Tower, Box 21598, Kitwe, kapena ku keyala yoyenera pandandanda ya patsamba 2.