Kodi Mungakonde Kuchezeredwa?
Ngakhale m’dziko lino lodzala ndi mavuto, mungakhoze kupeza chimwemwe kuchokera m’chidziŵitso cholongosoka cha Baibulo chonena za Mulungu, Ufumu wake, ndi chifuno chake chabwino kwambiri kaamba ka anthu. Ngati mungakonde chidziŵitso chowonjezereka kapena ngati mungakonde kuti wina abwere kudzachita nanu phunziro Labaibulo lapanyumba laulere, chonde lemberani ku Watch Tower, Box 21598, Kitwe, kapena ku keyala yoyenerera yondandalitsidwa patsamba 2.