Zisonyezero za Nkhani za mu Nsanja ya Olonda za 2001
Zosonyeza deti la kope lopezekamo nkhaniyo
BAIBULO
Buku Lokhala ndi Mabuku Onse a M’Baibulo, 5/1
Cyril ndi Methodius—Otembenuza, 3/1
Kuyamikira Baibulo la New World Translation, 11/15
Kumvetsa Baibulo, 7/1
Mipukutu ya ku Nyanja Yakufa, 2/15
N’kuphunziriranji Baibulo, 7/1
MAFUNSO OCHOKERA KWA OŴERENGA
Kodi akristu oona ayenera kuchiona motani chizoloŵezi chofala chopatsana ulere mapulogalamu ogulitsa a pakompyuta? 2/15
Kodi Danieli anali kuti pamene Ahebri atatu aja anawayesa kuti alambire fano lagolide? (Da 3), 8/1
Kodi kudzoza “Malo Opatulikitsa” kunachitika liti? (Da 9:24), 5/15
Kodi kulambira Yehova “mumzimu” kumatanthauzanji? (Yoh 4:24), 9/15
Kodi njoka ija m’munda wa Edene inalankhula motani? 11/15
Kodi Tiyenera Kupempherera Munthu Wochotsedwa? (Yer 7:16),12/1
Kodi Yehova anapangana naye pangano Abrahamu ali ku Uri kapena ku Harana? 11/1
Kodi Yobu anavutika kwa nthaŵi yaitali motani? 8/15
Kulowa mpumulo wa Yehova (Aheb. 4:9-11), 10/1
“Kupembedza mafano kosaloleka,” (1Pe 4:3), 7/15
Mitengo yonyamulira likasa la chipangano (1Maf.8:8), 10/15
“Miyamba” (2Pe 3:13) ndi “kumwamba” (Chiv. 21:1), 6/15
Mkazi wachikristu ndi zochitika za maholide, 12/15
N’chifukwa chiyani kuli kofunika kwa Akristu kuulula machimo awo kwa akulu mu mpingo? 6/1
Zinthu zonse zinalengedwa “kwa” Yesu motani? (Akol 1:16), 9/1
MBIRI YA MOYO WANGA
Anapirira ‘Kufikira Chimaliziro’ (L. Swingle), 7/1
Kuchirikizidwa ndi Yehova (F. Lee), 3/1
Kukatumikira Kulikonse Kumene Ndinkafunika (J. Berry), 2/1
Kutsatabe Njira ya Yehova (L. Valentino), 5/1
Kutumikira ndi Moyo Wonse Mosasamala Kanthu za Mayesero (R. Lozano), 1/1
Kuunika Kwauzimu Kukuwala ku Middle East (N. Salem), 9/1
Kuvomera Yehova Akamatipempha (M. Zanardi), 12/1
Moyo Waulemerero Potumikira Yehova (R. Kurzen), 11/1
Ndimayamikira Chifukwa Chokumbukira Zinthu Zamtengo Wapatali! (D. Caine), 8/1
Tinamuyesa Yehova (P. Scribner), 7/1
Tinkachitira Zinthu Limodzi (M. Barry), 4/1
Wosangalala ndi Wothokoza Ngakhale pa Vuto Losautsa Mtima (N. Porter), 6/1
“Yehova Wandichitira Zabwino Zambiri!”(K. Klein), 5/1
Zochitika Zosayembekezeka (E. & H. Beveridge), 10/1
MBONI ZA YEHOVA
Analandira Satifiketi Chifukwa cha Kuchita Bwino (Congo [Kinshasa]), 8/15
Anapambana Chizunzo cha Nazi, 3/15
Apambana Mlandu M’khoti Lapamwamba la Federal Constitution (Germany), 8/15
Dokotala wa Maso Afesa Mbewu (Ukraine, Israel), 2/1
France, 8/15, 9/1
Kale Tinali Mimbulu—Tsopano Ndife Nkhosa! 9/1
Kenya, 2/15
Kodi Ntchito Iyi Ingakhale Yabwino Kwambiri kwa Inu? (Utumiki wa pa Beteli), 3/15
Kumaliza Maphunziro a Gilead, 6/15, 12/15
Kusamalirana Muubale Wapadziko Lonse (Othawa Nkhondo), 4/15
Kuthandiza Achinyamata, 7/15
Madzi Opatsa Moyo ku Andes, 10/15
Misonkhano ya Chigawo ya “Akuchita Mawu a Mulungu,” 1/15
Misonkhano ya Chigawo ya “Aphunzitsi a Mawu a Mulungu,” 2/15
Misonkhano Yaikulu Ndi Umboni Wosangalatsa wa Ubale Wathu, 9/15
Mmene Bungwe Lolamulira Limasiyanirana ndi Bungwe Lalamulo, 1/15
Msonkhano Wapachaka wa 2000, 1/15
“Ntchito Yaukatswiri” (Seŵero la Pakanema), 1/15
Sitinali Tokha Pamene Chikhulupiriro Chathu Chinali Kuyesedwa (Magazi), 4/15
‘Thokozani Mboni za Yehova Chifukwa cha Ufulu Wachipembedzo,’ 5/15
“Tidzaonana mu Ufumu wa Mulungu” (F. Drozg), 11/15
Timachita Zonse Zomwe Tingathe! (Amishonale), 10/15
“Tsiku Lokambirana za Zipembedzo” (Sukulu za ku Poland), 11/1
MOYO NDI MIKHALIDWE YACHIKRISTU
Anthu Sakumvetsetsani? 4/1
Chikhulupiriro Chenicheni, 10/1
Gonjetsani Zinthu Zokulepheretsani Kupita Patsogolo, 8/1
Kodi Mulidi Ololera? 7/15
‘Kugwiritsa Ntchito Nthaŵi Moyenera,’ 5/1
Kukayika, 7/1
Kukulitsa Khalidwe Labwino, 1/15
Kulapa, 6/1
Kumvera—Phunziro Lofunika Paubwana, 4/1
Kupeŵa Matenda a Mtima Wauzimu, 12/1
Kupitirizabe Polefulidwa! 2/1
Kusankha Mwanzeru, 9/1
Kuthandiza Akazi Amasiye, 5/1
Kwaniritsani Zomwe Ana Anu Amafunikira! 12/15
Limbikitsani Chikhulupiriro mwa Yehova, 6/1
‘Madalitso Ali pa Wolungama,’ 7/15
“Madalitso a Yehova Alemeretsa,” 11/1
“Motero Thamangani,” 1/1
Mumatani Pakachitika Chinyengo, 11/15
Mungachite Moyenera Ngakhale Sanakulereni Bwino, 4/15
‘Ndi Nzeru Masiku Athu Adzachuluka’ (Miy. 9), 5/15
Samalirani Ana ndi Akazi Amasiye, 6/15
Tetezani Chikumbumtima, 11/1
Udani—Woyenera ndi Wosayenera, 2/15
‘Wodala Munthu Wopeza Nzeru’’ (Miy. 8), 3/15
Yendani ‘M’njira Yoongoka’ (miy. 10), 9/15
Zomwe Munazoloŵera Kuchita, 8/1
Zoyenera Kuchita Ngati Mukuvutika Maganizo, 4/15
NKHANI ZAZIKULU ZOPHUNZIRA
Abrahamu Anali Chitsanzo cha Chikhulupiriro, 8/15
Anthu Obwezeretsedwa a Yehova Akum’tamanda Padziko Lonse Lapansi, 2/15
Chikristu Choona Chikupambana! 4/1
Chipulumutso Kwa Osankha Kuunika, 3/1
Chisangalalo Kwa Oyenda M’kuunika, 3/1
‘Funafunani Mtendere ndi Kuulondola,’ 9/1
Funafunani Yehova Lisanadze Tsiku La Mkwiyo Wake, 2/15
Ganizirani Ntchito Zodabwitsa za Mulungu, 4/15
Khalanibe Osasunthika Ngati Oona Wosaonekayo! 6/15
Khalani Ndi Chikhulupiriro Monga cha Abrahamu! 8/15
Khalani ndi Mtima woopa Yehova, 12/1
Khalani ndi Mtima Wovomerezeka kwa Yehova, 10/15
Kodi Chikondi Chanu N’chosefukira Motani? 1/1
Kodi Madalitso A Yehova Adzakupezani? 9/15
Kodi Mtendere wa Kristu Ungachite Motani Ufumu M’mitima Yathu? 9/1
Kodi Mukuchita Mogwirizana Ndi Kudzipatulira Kwanu? 2/1
Kodi Mutha “Kusiyanitsa Chabwino ndi Choipa”? 8/1
Kodi Mwana “Wosakaza” Mungamuthandize Bwanji? 10/1
Kodi Mwapanga Choonadi Kukhala Chanuchanu? 2/1
Kondwerani ndi Mulungu Wachimwemwe, 5/1
Kondwerani Nthaŵi Zonse Potumikira Yehova, 5/1
Kondwerani Pakuti Mwadziŵa Yehova, 7/1
Kugonjetsa Kufooka Kwaumunthu, 3/15
Kulani M’chikondi, 1/1
Kumanga Banja Lolimba Mwauzimu, 5/15
Kupita Patsogolo Kukagonjetsa Komaliza! 6/1
Limbikirani Ntchito Yotuta! 7/15
Madalitso A Yehova Amatilemeretsa, 9/15
Malangizo a Mulungu Othandiza Posankha Wokwatirana Naye, 5/15
Mankhwala Omwe Angathandize Kuthetsa Nkhaŵa, 12/15
‘Mawu a Yehova Anapitirizabe Kukula,’ 4/1
Musakhale Akumva Oiŵala, 6/15
Musasiye Kuchita Zabwino, 8/15
Ndani Adzatisiyanitsa ndi Chikondi cha Mulungu? 10/15
“Ngati Mulungu Ali ndi Ife, Adzatikaniza Ndani?” 6/1
Onetsani Kuti Mukupita Patsogolo, 8/1
Opani Yehova ndi Kusunga Malamulo Ake, 12/1
Oyang’anira ndi Atumiki Otumikira Amaikidwa Mwateokalase, 1/15
Pezani Chimwemwe mwa Kukhala Wopatsa! 7/1
“Phunzirani kwa Ine,” 12/15
Samalirani Mzimu ndi Kukhala ndi Moyo! 3/15
Sangalalani Ndi Ntchito Yotuta! 7/15
Tamandani Yehova Chifukwa cha Ntchito Zake Zazikulu! 5/15
Taonani Wochita Zinthu Zodabwitsa! 4/15
Tchinjirizani Mtima Wanu, 10/15
Tsanzirani Yehova Pophunzitsa Ana Anu, 10/1
Tsiku la Yehova Lopereka Chiŵeruzo Layandikira! 2/15
‘Valani Kuleza Mtima,’ 11/1
Yehova Amatidziŵitsa Kuŵerenga Masiku Athu, 11/15
Yehova Ndi Mulungu Woleza Mtima, 11/1
Yehova Ndiye Pothaŵirapo Pathu, 11/15
Yenderani Limodzi ndi Gulu la Yehova, 1/15
NKHANI ZOSIYANASIYANA
Ahasimoni, 6/15
Asikuti, 11/15
Chikhulupiriro cha Nowa Chimatsutsa Dziko Lapansi, 11/15
Chimwemwe, 3/1
Chitetezo M’dziko Loopsali, 2/1
Chokhalitsa Kuposa Golide, 8/1
Enoke Anayenda ndi Mulungu, 9/15
“Khalidwe Lobisika Lowononga Thanzi” (Zolaula za pa Intaneti), 4/15
Kodi Abambo a Tchalitchi Anachirikiza Choonadi cha Baibulo? 4/15
Kodi Chilipo Chimene Chingagwirizanitse Anthu? 9/15
Kodi Chofunika Kwambiri N’chiyani? 9/15
Kodi Mungakhulupirire Miyezo ya Ndani? 6/1
Kodi Mungapange Dziko Lapansi Kukhala Malo Abwinopo? 10/15
Kodi Munthu Akamwalira Amakhala ndi Moyo Kwinakwake? 7/15
Kukhulupirira Mizimu, 5/1
Kuona Ndalama M’njira Yoyenera, 6/15
Kuvutika, 5/15
Lamulo la Chikhalidwe Likugwirabe Ntchito, 12/1
Mabala a Nkhondo, 1/1
‘Mankhwala Opaka M’maso Mwanu!’ 12/15
Maziko a Zimene Mumakhulupirira, 8/1
Mdyerekezi, 9/1
Mitengo Imene Imakhalitsa, 7/1
“Mitsempha Yako Idzalandirapo Moyo,” 2/1
‘M’kuunika Kwanu Tidzaona Kuunika,’ 12/1
Mmene Mungapambanire Paunyamata Wanu, 8/15
Mutha Kukhala ndi Chikhulupiriro Chenicheni, 10/1
Mzimu Wosafa? 7/15
“Ndikachita Apilo kwa Kaisara!”
Opaleshoni Yopanda Magazi, 3/1
Origen—Kodi Chiphunzitso Chake Chinakhudza Tchalitchi Motani? 7/15
Paradaiso Wauzimu, 3/1
Paulo Alinganiza Zopereka Zothandizira Oyera Mtima Pa Mavuto, 3/15
‘Taonani Khamu Lalikulu!’ 5/15
Uthenga Wabwino wa Ufumu, 4/1
Yamikirani Ndipo Sangalalani, 9/1
Zinthu Zowononga Mitengo, 11/1
Zomwe Tingaphunzire ku Mtengo wa Kanjedza, 10/1
OLENGEZA UFUMU AKUSIMBA
2/1, 4/1, 5/1, 6/1, 8/1, 10/1, 12/1
YEHOVA
Limbikitsani Chikhulupiriro mwa Yehova, 6/1
“Madalitso a Yehova Alemeretsa,” 11/1
YESU KRISTU
Kodi Yesu Amapulumutsa Motani? 11/15
Kuuka, 3/15
Yesu Weniweni, 12/15